Pular para o conteúdo
Publicidade

Romanos 14

5 Mundhu wakhoza kuganizila kuti siku lakuti ni lalikulu kupunda kupitilila lina, mundhu mwina wakhoza kuganizila kuti siku zonjhe ni sawa. Kila mundhu wachate umo njelu yake ikhulupilila 6 Mundhu uyo waona kuti siku limojhi ni lalikulu kupitilila lina, wachita chimwecho kwa kwaalemekeza Ambuye. Nde amuyamika Mnungu kwa chakudya. Chimchijha nawo yawo akana kudya chakudya chakuti achita chimwecho ndande ya Ambuye. Nawo amuyamika Mnungu.

Veja também