10 Yapo tidali tikali adani a Mnungu, Mnungu wadachita ubwenji ni ife kwa njila ya nyifa ya mwana wake. Ndande chipano takhala abwenji wa Amnungu, ndiipo tikhoza kupheza uzene kuti Atate siatiombole kuchokela ku mbhwayi yake, pakuti Yesu ni umoyo masiku yonjhe.