Pular para o conteúdo
Publicidade

Romanos 7

4 Mchimwecho acha abale wanga, anyiimwe mdalekeledwa kuchokela thauko ngati umo mmakhalila kale, anyiimwe ni malo ya thupi la kilisito, chipano muli wa yujha wadahyukichidwa kuti mkhoze kuchita vichito vabwino ndande ya Mnungu. 5 Pakuti yapo timakhala ngati wandhupe umo akhalila, makumbilo yayo yadasongezeledwa ni machimo yamachita njhito mmatupi yathu, ni kupeleka nyifa. 6 Kalepo tidamangidwa ni thauko, nambho saino tamwalila pamojhi kilisito, mchimwecho tamasulidwa kuchokela mthauko. Chipano sitimtumikila Mnungu kwa njila ya kale ya kugwila thauko ilo lidalembedwa, nambho timtumikila Mnungu kwa njila ya chipano ya kuchogozedwa ni mzimu wa wake.

Veja também