15 Pakuti simdalandile Mzimu wakukuchitani anyiimwe akapolo ni kukupachani mandha, nambho mwalandila Mzimu wakukuchitani anyiimwe wana a Mnungu, ni mwa Mzimu umeneo ife timtana Mnungu, "Aba" Mate yake, "Tate!" 16 Nawo Mzimu wene ulangiza mkati mwa mitima yathu, kuti ife ni wana a Mnungu.