Pular para o conteúdo
Publicidade

2 Coríntios 6

4 Mmalo mwake, kwakila kandhu tijhilangize kuti ife atumiki a Mnungu, kwa kila kandhu, kwa kulimba mtima kupunda kwa mavuto, machaucho ni kulaga, 5 tidabulidwa ni kumangidwa mndende ni kwa kukuwidwa pa ndhandala pakuchita njhito zolimba zolemecha, tachezelela ni kukhala popande kudya. 6 Tijhilangiza kukhala atumiki a Mnungu kwa mtima woyela, kwa malango, kwa kulimba mtima ni kwa ubwino, kwa Mzimu wa Mnungu ni kwa chikondi chopande ugunghuli, 7 kwa mau la uzene ni kwa mbhavu ya Mnungu. Kuvomelezeka ni Mnungu nde chida chathu cha kukengelela ni kuhundukila. 8 Ife timtumikila Mnungu wandhu akati lemekeza kapina kutudelela, tilaumidwa ni kutielekela. Tionekana amthila kumbe tikamba zene, 9 ngati osajhiwika kumbe tijhiwika kupunda, tioneka ngati omwalila kumbe ife amoyo. 10 Ingakhale talangidwa, sitidaphedwe, ingakhale tionekana tali ni chisoni, tikondwa, ingakhale tili osauka nambho tachita ambili kukhala opata, tioneka wandhu opande kandhu, kumbe tili ni kila kandhu.

Veja também