Athandhizi saba a atumwi asanghidwa
1 Yapo idapita ndhawi yochepa, chiwelengelo cha wandhu chimayendekela kukula kupunda, padachokela madandaulo pakati pa oyaluzidwa a Yesu yao amakamba mkambo ya chigiliki ni oyaluzidwa a Yesu yao amakamba mkambo wa Chiebulaniya, kuti wachikazi wao yawo asiidwa ni wachimuna wao adaiwalidwa pa kugawa chakudya cha kila siku.
6 Adaimika wandhu ameneo pachogolo pa atumwi, adaapembhela ni kwapacha mwawi kwa kwaikila manja.