Pular para o conteúdo
Publicidade

Aloma 7

2 Kwa chifani, wamkazi uyo wakwatiwa wamangidwa ni thauko ndhawi yonjhe yapo mmunake wakhala wamoyo, nambho mmunake wakamwalila, thauko limenelo silimmanganjho wamkazi mmeneyo. 3 Chimwecho wamkazi mmeneyo wakakwatiwa ni wammuna mwina ndhawi iyo mmunake wali wamoyo, siwatanidwe wachighololo. Nambho mmunake wakamwalila, wamkazi mmeneyo siwamangidwanjho ni thauko la ukwati, ni wakakwatiwa ni wammuna mwina siwatanidwa wachighololo.

Estes versículos te tocaram? Ore agora!

+581 estão orando agora.

Junte-se à corrente de oração.

Veja também