Pular para o conteúdo
Publicidade

1 Akolinso 16:1-3

NTNYBL2025 Nyanja

Kwathangatila wandhu amkhulupila Kilisito

1 Chipano, nghani ya kuchocha njhembe ndande ya wandhu a Mnungu, chitani ngati umo nidaatumizila gulu la wandhu amkhulupilila Yesu aku Galatia. 2 Kila jumapili, kila mmojhi wanu wapatule ndalama ni kuzisunga, kuchokana ni kupata kwake, dala sikudakhala ni vuto la kuzipata ndalama za kunipacha. 3 Chimwecho yapo sinijhe kwanu, sinaatume anyiwajha simwasanghule pakati panu apeleke kalata ku Yelusalemu ni ndalama zijha mwasunga.

Em outras traduções

  1. TCCL Abra a Palavra de Deus em Chichewa Contemporâneo

    1 Tsopano za zopereka zothandiza anthu a Ambuye a ku Yerusalemu. Muchite zomwe ndinawuza mipingo ya ku Galatiya kuti ichite. 2 Pa tsiku loyamba la sabata lililonse, aliyense wa inu azipatula ndalama molingana ndi zomwe wapezera. Asunge, kuti ndikabwera pasadzakhalenso msonkhamsonkha. 3 Pamenepo, ndikadzafika, ndidzawapatsa makalata a umboni anthu amene mudzawasankhe ndi kuwatuma kuti akapereka mphatso zanu ku Yerusalemu.

Direitos das traduções citadas

Estes versículos te tocaram? Ore agora!

+581 estão orando agora.

Junte-se à corrente de oração.