Pular para o conteúdo
Publicidade

2 Coríntios 9

6 Zindikilani mau yaya, uyo wavyala pang’ono wakolola pang’ono, uyo wavyala zambili wakolola zambili. 7 Kila mmojhi, chipano wachoche ngati umo wakhozela, kwa mtima asati kuchocha kwa kudandaula kapina kukakamizidwa, pakuti Mnungu wamkonda yujha wachocha kwa mtima kokondwela. 8 Mnungu wakhoza kukupachani anyiimwe kupitilila yayo muyafuna, dala mkhale ni kila chindhu icho muchifuna siku zonjhe, dala mpunde kuthangatila kwa kila njhito iyo ili yabwino. 9 Ngati umo yalembedwa mmalembo ya Mnungu,

"Iye wachocha kwa ubwino,

wapacha osauka,

ubwino wake ulama muyaya."

10 Mnungu uyo wampacha mlimi mbeu ndande yovyala niuyo wampacha chakudya, siwakupacheni mbeu izo muzifuna, siwazichite zimele, zikule ni kukupachani vokolola vambili va ubwino wanu. 11 Iye siwakuchiteni kupata kwa kila kandhu, dala kwa ubwino wanu wandhu amuyamike Mnungu, kupitila ife. 12 Njhito iyi yabwino iyo muichita siithangatila vofunika va wandhu a Mnungupe, nambho siichite wandhu ambili amuyamike Mnungu.

Veja também