Pular para o conteúdo
Publicidade

Atos 15

Poolo ni Banaba apatulana

36 Pambuyo pa masiku yochepa, Poolo wadamkambila Banaba, "Tibwelele tikaapenye achabale wathu mmijhi yonjhe umo tidalalikila mawu la Ambuye kuti tikaone umo ayendekela." 41 Iye wadapita pakati pa Siliya ni Kilikiya, uku ni waathila mtima gulu la wandhu amkhulupilila kilisito amalo ya meneyo.

Veja também