15 Iye pamojhi ni wandhu wonjhe yawo amakhala mnyumba mwake adabatizidwa. Ndiipo wadatitana kunyumba kwake, niwakamba, "Ngati muuona kuti ine nakhulupilila Ambuye Yesu, majhani kukhomo kwanga mkhale." Wadatipembha kupunda tipite kukhomo lake.
Publicidade