Poolo waona maloso
6 Poolo ni achanjake adapita mmijhi ya Filigia ni Galatiya, ndande Mzimu Woyela udaakaniza kulalikila uthenga wa Bwino ku jhiko la Asia. 7 Adafika mmalile mwa mujhi wa Musiya. Adayesa kulowa ku mujhi wa Bisiniya, nambho mzimu wa Yesu udaakaniza kulowa mmenemo.