Pular para o conteúdo
Publicidade

Atos 8

30 Ndiipo Filipo wadaithamangila ni kuiwandiikila ijha ngolo ni wadamuvela wamkulu yujha niwasoma chikalakala cha mlosi Isaya. Filipo wadamfunjha, "Bwanji, uvananavo ivo usoma?"

31 Wamkulu yujha wadayangha, "Nivananavo bwanji ngati palibe mundhu wonifotokozela ivo valembedwa?" Chimwecho wadamkambila Filipo wakwele mungolo mujha nikukhala pamojhi ni iye. 32 Wamkulu mmeneyu wamasoma malembo yaya,

"Wadachogozedwa ngati mwana mbelele iyo ipita kuphedwa,

wadakhala chete ngati mwana mbelele yapo wadulidwa mabweya,

iye siwadachoche mvekelo ata pang’ono.

Veja também