Pular para o conteúdo
Publicidade

Vichito 8

32 Wamkulu mmeneyu wamasoma malembo yaya,

"Wadachogozedwa ngati mwana mbelele iyo ipita kuphedwa,

wadakhala chete ngati mwana mbelele yapo wadulidwa mabweya,

iye siwadachoche mvekelo ata pang’ono.

33 Wadalengechedwa njhoni ni kumanidwa kuvomelezeka.

Palibe uyo siwakhoze kukamba kuusu mbadwa wake,

pakuti umoyo wake wachochedwa pajhiko."

34 Yujha wamkulu wadamfunjha Filipo, "Nipembha unikambile, uyu mlosi wakamba nghani za yani? Nghani zake mwenewake kapina nghani za mundhu mwina?" 35 Ndiipo Filipo wadayamba kumkambila kupitila yajha malembo wamayasoma, pakumkambila Uthenga wa Yesu.

Estes versículos te tocaram? Ore agora!

+581 estão orando agora.

Junte-se à corrente de oração.

Veja também