36 Mmujhi wa Yopa mudali wamkazi mmojhi wokhulupilila uyo wamatanidwa Tabisa, pa Chiyunani Dokasi, mate yake, Ngolombwa. Wamkazi mmeneyo wamachita vabwino ni kwaathangatila wandhu wosauka siku zonjhe. 37 Ndhawi ijha iye wadadwala ni kumwalila. Thupi lake lidachukidwa ni kuliika kuchumba cha golofa. 38 Mujhi wa Yopa siudali patali ni mujhi wa Lida, wokhulupilila aku Yopa yapo adavela kuti Petulo wadali mumujhi wa Lida, adaatuma athenga awili kwa iye nikumpemba, niakamba, "Chonde ujhe kwathu sazino." 39 Chimwecho Petulo wadachoka, wadapita pamojhi ni athenga wajha. Yapo wadafika ku Yopa, wadapelekedwa golofa ku chumba chijha, uko wachikazi ambili yawo afedwa wachimuna adalizungulila thupi. Anyiiwo amalila ni kumlangiza Petulo malaya ni makhoti yayo wadakonja Dokasi yapo wadali wamoyo.