7wadamkambila, "Pita ukasambe kuthiwi la Siloamu." Mawu Siloamu mate yake Uyo watumidwa. Chimwecho wadapita kusamba, wadabwela uku ni wapenya.
14Siku ilo Yesu wadamlamicha yujha sapenya lidali Siku lo Pumulila.
32Kuyambila mmayambo mwa jhiko sikudavekelepo paliponjhe kuti kuli mundhu wamlamicha mundhu uyo wabadwa sapenya kupenya.