4 Anyiiwo adamuyahga, "Musa wadaagiza wammuna wakhoza kulemba talaka ni kumsiya wamkazi."
5 Yesu wadaakambila, "Musa wadakulembelani lamulo limenelo ndande simuyaluzika. 6 Nambho, kuyambila kuumbidwa kwa jhiko, Mnungu wadaumba wamuna ni wamkazi. 7 Chimwecho, wamuna siwasiye atate wake ni amake ni kulunjana ni mkazake, 8 ni anyiiwo awili sakhale thupi limojhi. Chipano anyiiwo osati awilinjho, nambho ni thupi limojhi. 9 Chimwecho, icho wachilunjanicha Mnungu, mundhu siwadachisiyanicha."