Yesu wamlamicha mundhu pa Siku lo Pumulila
1 Ndiipo Siku lina lo Pumulila, Yesu wadalowanjho mnyumba yokomanilana Ayahudi, ni mujha mkati kudali ni mundhu uyo wali ni jhanja lovuwala. 2 Mmenemo, kudali Afalisayo akumojhi yawo amampenya amuone ngati samlamiche mundhu Siku lo Pumulila apate ndande ya kumgwila. 3 Yesu wadamkambila yujha mundhu wadali ni jhanja lovuwala, "Majha pano pakatikati." 4 Ndiipo wadaafunjha wandhu, "Bwanji, mathauko ya Musa yatifuna tichite chiyani pa Siku lo Pumulila? Bwanji, kuchita vabwino kapina kuchita voipa? Kuuwombola umoyo wa mundhu kapina kuupha?" Nambho anyiiwo adakhala chete. 5 Yesu wadaapenya wonjhe kwa mbhwayi, pamenepo wadaona chisoni mumtima mwake ndande ya kosakhulupilila kwawo. Ndiipo wadamkambila yujha mundhu, "Tambasula jhanja lako." Ni yujha wovuwala wadatambasula jhanja lake, ni kulama.