Pular para o conteúdo
Publicidade

Maluko 3

22 Oyaluza athauko la Musa, yawo adachokela ku Yelusalemu, adakamba, "Wachogozedwa ni Belizabuli wamkulu wa viwanda, nde uyo wampacha mbhavu zotopola viwanda." 23 Yesu wadaatana ni kwaakambila kwa chifani, "Bwanji, Satana wakhoza kujhitopola mwenewake? 24 Ufumu uliwonjhe ukapatukana ni kubulana, ufumu umenewo siukhoza kulimba. 25 Ikakhala wandhu a nyumba imojhi apatukana achinawene magulumagulu yayo yachuchana, nyumba imeneyo siikhoza kulimba. 26 Ngati ufumu wa Satana wapatukana magulumagulu siukhoza kulimba, ni siugwe."

27 "Palibe mundhu wakhoza kuhundukila nyumba ya mundhu uyo wali ni mbhavu ni kumlanda chuma chake popande kummanga. Wakammanga ndeyapo siwakhoze kumlanda chuma chake."

28 "Zenedi nikukambilani, machimo yonjhe yayo achita wandhu, ni kukafula kwawo konjhe, Mnungu siwalekelele. 29 Nambho mundhu waliyonjhe uyo wamkafula Mzimu Woyela, kukafula kwake sikulekeleledwa muyaya. Ndande wachita machimo ya muyaya." 30 Yesu wadakamba chimwecho ndande anyiiwo amakamba, "Wali ni chiwanda."

Veja também