Pular para o conteúdo
Publicidade

Maluko 4

3 "Vechelani! Wovyala wadapita kumijha mbewu. 4 Yapo wamamijha mbewu, zina zidagwela panjila, mbalami zidajha ni kuzidya. 5 Zina zidagwela pamwala yapo palibe dothi lambili, zidamela chisanga ndande dothi lidali lochepa. 6 Jhuwa yapo lidatuluka, lidaphyeleza mimela, pakuti mizo yake siidapite panjhi. 7 Zina zidagwela pa minga, nazo zijha minga zidakula ni kuzizinga zijha mimela, ni siidabale njele yaliyonjhe. 8 Zina zidagwela pa dothi la chaila, zidamela, ni zidakula ni kubala, imojhi idabala njele selasini, ina adabala njele sitini, ni ina adabala njele miya." 9 Ndiipo Yesu wadakambila, "Mchate icho mkambidwa!"

Veja também