Pular para o conteúdo
Publicidade

1 Coríntios 1

13 Bwanji, Kilisito wadajhipatula magulumagulu? Bwanji, Poolo nde uyo wadapachikidwa pa mtanda ndande yanu? Bwanji mudabatizidwa ngati oyaluzidwa a Poolo?

14 Naayamika Amnungu pakuti sinidambatize waliyonjhe pakati panu, nambho Kilisipo ni Gayo pe. 15 Chimwecho palibe uyo wakhoza kukambi wabatizidwa kuti wakhale oyaluzidwa wanga. 16 Nakumbukila, nidambatiza Sitefano ni wandhu amnyumba mwake, nambho sinikumbukila ngati nidambatiza mundhu mwina waliyonjhe. 17 Kilisito siwadanitume kubatiza. Wanituma kulalikila Uthenga Wabwino, nilalikile popande kukhulupilila mawu ya hekima za wandhu, dala mbhavu ya nyifa ya Kilisito pamtanda siidaoneka yopandemate.

Veja também