Pular para o conteúdo
Publicidade

1 Akolinso 5

Chigololo chiwananga gulu lamkhulupilila Yesu

1 Navela kuti kwanu kuli chigololo, ni chigololo icho sichidakhalepo ata kwa wandhu yao siamjhiwa Mnungu, nakambilidwa pakati panu mmojhi wakhala ni wamkazi wa atate wake. 2 Namwe mujhidama, bwanji ata simudandaula, nikumchocha pakati panu mmeneyo wachita chigololo chimenecho.

Estes versículos te tocaram? Ore agora!

+581 estão orando agora.

Junte-se à corrente de oração.

Veja também