10 Chimwecho chisoni icho chichokana ni umo wafunila Mnungu chichita wandhu asiye machimo ni kuomboledwa, ni sichachita wandhu akaule. Nambho chisoni icho chichokana ni jhiko chipeleka nyifa. 11 Chipano mwaona chisoni icho chiyambichidwa ni Mnungu umo chapelekela phindhu kwanu yokhala wandhu abidii, juhudi iyo mwichita kujhiteteza, kupweteka kwanu, mandha yanu, chikondi chanu, kumbilo lanu lochochocha chilango icho chifunika. Kwa yamaeneyo yonjhe mlangiza kuti mlibe cholakwa pa chindhu ichi.
Publicidade