38 Chimwecho, achaabale wathu a Izilaeli mujhiwe kuti kwa njila ya Yesu, uthenga wa kulekeleledwa machimo ulalikidwa kwanu. 39 Mundhu waliyonjhe uyo wamkhulupilila Kilisito siwalekeleledwe machimo yake. Chindhu icho sichidakakhozeka kwa kulemekeza thauko la Musa.
Publicidade