Timoseo walunjana ni Poolo ni Sila
1 Ndiipo Poolo wadafika ku Delibe ni Lisitila, uko wamakhala ochatila mmojhi wa chi Yahudi uyo wadamkhulupila Yesu wamatanidwa Timoseo, uyo amake adali ochatila wa Chiyahudi, nambho atate wake adali Agiliki. 3 Ndiipo Poolo wamafuna kumtenga Timeseo kuti wachatane ni iye, chimwecho wadamchita mdulidwe. Iye wadachita chimwecho ndande Ayahudi wonjhe yawo amakhala malo yameneyo amajhiwa kuti atate a Timoseo ni Agiliki.