26 Iye wadayamba kukamba popande mandha mnyumba zokamanilana Ayahudi. Pulisila ni Akila yapo adamvela iye niwakamba, adamtenga kupita nayo kukhomo ni kumfotokozela bwino Malembo ya Mnungu yayo siwamayajhiwe.