17 Ambuye Amnungu akamba, ‘Pa masiku yothela,
sinapache wandhu wonjhe Mzimu wanga.
Wana wanu ni anamwali wanu sialosele,
anyamata wanu saone maloso,
azee wanu saalote maloto.
18 Yetu ata mbowa zanga waachimuna ni waachikazi,
sinapache Mzimu wanga pa masiku yameneyo,
anyiiwo siachoche ulosi.