23 Kuyambila mmayambo Mundhu wadafuna anyiimwe mumphe Yesu, ni anyiimwe mdampha kwa kwasiila wandhu woipa ampachike pamtanda. 24 Nambho Mnungu wadamhyukicha ni kumchocha kupweteka kwa nyifa. Pakuti siidakhozeke kuti mbhavu za nyifa zimmange iye ngati mundhu womangidwa mndende.