9 Nambho ata chimwecho, adachokela wandhu wina kuti achuchane ni Sitefano. Akumojhi wa wandhu ameneo adachokela ku nyumba yokomanilana Ayahudi iyo itanidwa, Nyumba ya ufulu. Wandhu ameneo adachokela ku Kilene ni a Isikandiliya, wandhu wina adachokela ku Kilikiya ni ku Asiya. 11 Chimwecho adaaguza wandhu kuti akambe, "Ife tidamuvela niwakamba mawu yomtukwana Musa pamojhi ni Mnungu!"