Pular para o conteúdo
Publicidade

Marcos 13

9 "Nambho anyiimwe mkhale maso. Pakuti wandhu saakugwileni ni kukupelekani ku bwalo la milandu. Saakubuleni ku nyumba zokomanilana Ayahudi. Simpelekedwe kwa alamuli ni mafumu ndande ya ine, kuti mwalalikile Uthenga Wabwino. 10 Mathelo yakali osafike, Uthenga Wabwino ufunika ulalikidwe mmayiko yonjhe.

Veja também