Chifani cha mbewu ya haladali
30 Yesu wadafunjhanjho, "Bwanji, Ufumu wa Mnungu ulingana ni chiyani? Bwanji, tiufotokoze kwa chifani chanji? 32 Nambho ikavyalidwa, imela ni kukhala mtengo waukulu kupitilila mitengo yonjhe ya mmunda, ni ndhawi zake zikhala zazikulu, ni mbalame zikhoza kumanga visa mndhawi zake"