10 Nambho kwa anyiwajha akwata nili ni lamulo. Wamkazi siwadasiyana ni mmunake, 11 nambho ikakhala wamkazi wasiyana nimmunake, siwada kwatiwa, kapina wabwelelane ni mmunake, ni wammuna siwadalemba kalata ya kumsiya mkazake.
12 Nambho kwa wina, ine nikukambilani osati Ambuye akamba, ngati wammuna wali ni wamkazi, siwada khulupilile, ni wamkazi wavomela kukhala nayo siwadamsiya.