14 Kwa wammuna siwadakhulupile walandilidwa kwa Mnungu kwa kulunjana ni mkazake, ni wamkazi siwada khulupilile walandilidwa ni Mnungu kwa kulunjana ni wammuna wamkhulupilila Kilisito. Ngati siidakali chimwecho wana wanu sadakavomelezedwa ni Mnungu, kumbe chipano avomelezedwa kukhala wana a Mnungu.
Publicidade