15 Nambho, wammuna kapina wamkazi siwadakhulupile wafuna kumsiya mnjake uyo wakhulupilila, chimwecho wachite chimwecho. Pakuchita chimwecho, wamkazi kapina wammuna wakhulupila siwamangika ndande Mnungu watitana tikhale ni umoyo wa mtendele.
Publicidade
Publicidade