Pular para o conteúdo
Publicidade

1 Coríntios 7

3 Wammuna wachite umo ifunikila kwa mkazake, ni wamkazi wachite umo ifunikila kwa mmunake, ni kila mmojhi wamkwaniliche mnjake icho chifunika. 4 Wamkazi walibe lamulo pamwamba pa thupi lake, nambho mmunake wali nilamulo pamwamba pa thupi la mkazake, chinchijha wammuna nayonjho walibe lamulo pamwamba pathupi lake, nambho mkazake wali nilamulo pa mwamba pathupi la mmunake. 5 Msadamanana nambho ikakhala mwavomelezana dala mpheze ndhawi ya mapembhelo, ndiipo mbwelelenjho ili Mdani wa Mnungu siwadapheza kukuikani mmayeso ndande ya kulepela kuchekeleza mafuno yanu.

Veja também