Pular para o conteúdo
Publicidade

Atos 10

47 "Wandhu anyiyawa alandila Mzimu Woyela, ngati umo tidamlandilila ife. Bwanji, pali mundhu waliyonjhe uyo wakhoza kukaniza kuti saadabatizidwa kwa majhi?" 48 Chimwecho wadalamula kuti abatizidwe kwa jhina la Yesu Kilisito. Basi wandhu anyiwajha adampembha Petulo wakhale ni anyiiwo kwa masiku yochepa.

Veja também