Pular para o conteúdo
Publicidade

João 14

5 Tomaso wadamfunjha, "Ambuye, uko mpita ife sitikujhiwa, sitiijhiwe bwanji njila yopita kumeneko?"

6 Ndiipo Yesu wadamuyangha, "Ine namwene nde njila, naakambila wandhu uzene ni kwapacha umoyo wa muyaya. Palibe uyo wakhoza kupita kwa Atate ila kwanjila yanga.

Veja também