Pular para o conteúdo
Publicidade

Yohana 8:31-36

NTNYBL2025 Nyanja

Uzene siukulekeleleni

31 Ndiipo, Yesu wadaakambila Ayahudi yawo adamkhulupilila, "Mkayagwila mayaluzo yanga simukhale oyaluzidwa wanga azene. 32 Simuujhiwe uzene, ni uzene siukulekeleleni."

33 Nawo adayangha, "Ife mibadwa ya Ibulahimu, sitidakhalepo akapolo amundhu waliyonjhe. Ukamba bwanji kuti, ‘Sitilekeledwe?’"

34 Yesu wadayangha, "Uzene nikukambilani, uyo wachita machimo ni kapolo wa machimo. 35 Kapolo walibe pokhala polimba pakhomo, nambho mwana wali ni pokhala. 36 Mwana wakakuchitani mlekeleledwe simulekeleledwe zenezene.

Em outras traduções

  1. TCCL Abra a Palavra de Deus em Chichewa Contemporâneo

    31 Kwa Ayuda amene anamukhulupirira, Yesu anati, "Ngati inu mutsatira chiphunzitso changa, ndithu ndinu ophunzira anga. 32 Tsono mudzadziwa choonadi, ndipo choonadicho chidzakumasulani."

    33 Iwo anamuyankha Iye kuti, "Ife ndife zidzukulu za Abrahamu ndipo sitinakhalepo akapolo a wina aliyense. Kodi mukunena bwanji kuti, ‘Ife tidzamasulidwa?’ "

    34 Yesu anayankha kuti, "Zoonadi, Ine ndikukuwuzani kuti aliyense wochita tchimo ndi kapolo wa tchimolo. 35 Pajatu kapolo alibe malo wokhazikika mʼbanja, koma mwana ndi wa mʼbanjamo nthawi zonse. 36 Nʼchifukwa chake ngati Mwana adzakumasulani, mudzakhala mfulu ndithu.

Direitos das traduções citadas

Estes versículos te tocaram? Ore agora!

+581 estão orando agora.

Junte-se à corrente de oração.