Yakobo ni Yohana ampembha Yesu ukulu
35 Ndiipo Yohana ni Yakobo, wana wa Zebadayo, adamchata Yesu nikumkambila, "Oyaluza, kuli chindhu tifuna mtichitile." 36 Yesu wadaafunjha, "Mfuna nikuchitileni chiyani?" 37 Adamuyangha, "Yapo simkhale pampando wanu wachifumu pa ulemelelo wanu, tipembha mmojhi wakhale bendeka lanu la kumanjele, ni mwina bendeka lanu la kwene."