11 Yapo siakugwileni ni kukupelekani ku bwalo la milandu, msadaganizila chokamba. Ndhawi ikajha kambani chalinjhonjhe icho simpachidwe, pakuti osati anyiimwe simkambe nambho Mzimu Woyela.