Pular para o conteúdo
Publicidade

Marcos 6

48 Ndiipo, Yesu wadaaona oyaluzidwa wake niavutika kwa kupalasa nghafi, ndande mbhepo imaabula kwa mbhavu. Mmalengakucha, Yesu wadayendela oyaluzidwa wake uku niwayenda pamwamba pa majhi, wamafuna kwapitilila. 49 Yapo adamwona ni wayenda pamwamba pa majhi, amaganizila udali mzilimu, adabula pokhoso. 50 Pakuti wonjhe adamwona, ni adaopa. Yesu wadaakambila, "Jhitileni mtima! Ni ine! Msadaopa!" 51 Ndiipo wadakwela mboti umo adali woyaluzidwa, ni mbhepo idasiya, oyaluzidwa wake adazizwa kupunda,

Veja também