Yesu waapacha chakudya wandhu elufu zinayi
1 Pa masiku yameneyo, gulu lalikulu la wandhu lidapezananjho, ni adalibe chakudya. Ndiipo, Yesu wadaatana oyaluzidwa wake, ni kwakambila, 2 "Nialengela lisungu wandhu anyiawa, ndande akhala niine masiku yatatu ni alibe chindhu cha kudya. 3 Nikaasiya abwele mmakhomo yao uku ali ni njala, siakomoke mnjila ndande wina achokela kutali."
4 Oyaluzidwa wake adamfunjha, "Pano ni paphululu, sitipate kuti chakudya cha kwaapacha wandhu wonjhewa?" 5 Yesu wadaafunjha, "Muli ni mabumunda yangati?" Adamuyangha, "Tili ni mabumunda saba."
6 Yesu wadaakambila wandhu akhale panjhi. Wadayatenga yajha mabumunda saba, wadamuyamika Mnungu, wadaibandhula ni kwapacha oyaluzidwa wake wagawile wandhu, nawo oyaluzidwa wake adachita chimwecho. 7 Chimwechonjho adali ni njhomba zazing’onozing’ono zochepa. Yesu wadamuyamika Mnungu, ni chinchijha wadaakambila oyaluzidwa wake wagawile wandhu. 8 Wandhu adadya ni kukhuta. Ndiipo woyaluzidwa wake adakusa vakudya vidakhalila ni kujhaza miseche saba. 9 Ni wandhu yawo adadya adali ngati elufu zinayi. Ndiipo Yesu wadaalaila wandhu apite kumakomo yao,