Pular para o conteúdo
Publicidade

1 Coríntios 11

24 wadamuyamika Mnungu, wadaubandhula, wadakamba, "Ili nithupi langa, ilo lachochedwa ndande yanu. Chitani chimwechi kwa kunikumbukila." 25 Chimwechijha, pambuyo pakudya wadatenga chiko niwakamba, "Chikho ichi ni chipangano cha chipano cha Mnungu, chichimikizidwa kwa mwazi wanga. Chitani chimwechi kila yapo mkumwa, kwa kunikumbukila."

26 Pakuti kila yapo simujhidya bumunda ili ni kumwa mchikho ichi, muuzila wina Ambuye adafa ndande yanu mbaka yapo siwajhe. 27 Chimwecho, kila uyo wakudya bumunda la Ambuye, ni kumwa mchikho ichi ngati umo siifunikila, siwakhale wachita machimo kwa thupi ni mwazi wa Ambuye. 28 Ifunika, mundhu wajhipenyecheche mwene, ukali osadye bumunda ni kumwa mchikho.

Veja também