2 Ndiponjho ata ngati, nali ni mbhaso yolalikila Uthenga wa Mnungu, ni kujhiwa nghani zonjhe za Mnungu ni hekima zonjhe, atangati nali nichikhulupi chokwana mbaka kukhoza kuzula phili ngati nilibe chikondi ine asati kandhu.