14 Uyo walibe Mzimu wa Mnungu siwakhoza kulandila mbhaso ikujha kuchokela kwa Mzimu wa Mnungu. Mundhu mmeneyo siwakhoza kuva yameneyo, waona kuti vindhu vimenevo vilibe mate, ndande yake yavunukulidwa muchizimu. 15 Uyo wali ni Mzimu wa Mnungu, wakhoza kulamula ngati umo ifunika, nambho siwakhoza kulamulidwa ni wandhu wina. 16 Ngati umo yalembedwa mmalembo ya Mnungu,
"Yani wajhiwa maganizo ya Mbuye?
Yani wakhoza kumkambila Mnungu chindhu chochita?"
Nambho ife tili ni maganizo ngati Kilisito.