3 Wammuna wachite umo ifunikila kwa mkazake, ni wamkazi wachite umo ifunikila kwa mmunake, ni kila mmojhi wamkwaniliche mnjake icho chifunika. 4 Wamkazi walibe lamulo pamwamba pa thupi lake, nambho mmunake wali nilamulo pamwamba pa thupi la mkazake, chinchijha wammuna nayonjho walibe lamulo pamwamba pathupi lake, nambho mkazake wali nilamulo pa mwamba pathupi la mmunake.