Pular para o conteúdo
Publicidade

Yohana 10:3-5,14,27

NTNYBL2025 Nyanja

3 Mlonda wachakulila, ni mbelele zivela mvekelo wake, nayo wazitana mbelele kila imojhi kwajhina lake, ni kuzitulucha kubwalo. 4 Ndiipo wakatho zitulucha kubwalo wazichogolela mbelele, nazo zimchota, ndande ziujhiwa mvekelo wake. 5 Mbelele zimenezo sizikhoza kumchata mlendo, nambho sizimthawe ndande sizijhiwa mvekelo wake."

14 Ine ni owesa wabwino. Nizijhiwa mbelele izo zili zanga, ni mbelele zanga zinijhiwa ine,

27 Ngati mujha mbelele zivela mvekelo wa owesa wao, wandhu wanga achijhiwa icho nichikamba nane najhiwa ni akhala ochatila wanga.

Em outras traduções

  1. TCCL Abra a Palavra de Deus em Chichewa Contemporâneo

    3 Mlonda amamutsekulira khomo, ndipo nkhosa zimamvera mawu ake. Iye amaziyitana mayina nkhosa zakezo, nazitulutsa. 4 Akazitulutsa nkhosa zake zonse, iye amazitsogolera, ndipo nkhosa zakezo zimamutsata chifukwa zimadziwa mawu ake. 5 Koma nkhosazo sizidzatsatira mlendo. Izo zidzamuthawa chifukwa sizizindikira mawu a mlendo."

    14 "Ine ndine mʼbusa wabwino. Ine ndimazidziwa nkhosa zanga ndipo nkhosa zangazo zimandidziwa,

    27 Nkhosa zanga zimamva mawu anga, Ine ndimazidziwa, ndipo zimanditsata Ine.

Direitos das traduções citadas

Estes versículos te tocaram? Ore agora!

+581 estão orando agora.

Junte-se à corrente de oração.