28 Nambho mwana wamkulu yujha wadakwiya ni wadakana kulowa mnyumba. Ndiipo atate wake adatuluka kubwalo ni kumpempha kupunda. 29 Nambho iye wadayangha atate wake, ‘Vechelani! Nakutumikilani vyaka vonjhevi ni palibe siku ilo nakana kuchita icho munilamula, nambho simudanipachepo ata kamwana ka mbuzi kuti nichite phwando niachabwenji langa! 30 Nambho mwana wanu uyu uyo wawananga chuma chanu ni mahule, yapo wabwela pakhomo mwamphela njinda ya ng’ombe!’
Publicidade
Luka 15:28-30
NTNYBL2025 Nyanja
Em outras traduções
- TCCL Abra a Palavra de Deus em Chichewa Contemporâneo
28 "Mwana wamkulu anakwiya ndipo anakana kulowa. Chomwecho abambo ake anatuluka ndi kumudandaulira. 29 Koma iye anayankha abambo ake kuti, ‘Taonani! Zaka zonsezi ndakhala ndikukutumikirani kugwira ntchito yowawa ndipo palibe pamene sindinamvere malamulo anu. Koma inu simunandipatse ngakhale mwana wambuzi kuti ine ndichite phwando ndi anzanga. 30 Koma pamene mwana wanu uyu amene wawononga chuma chanu ndi achiwerewere wabwera ku nyumba, inu mwamuphera mwana wangʼombe wonenepa.’ "
Direitos das traduções citadas
Estes versículos te tocaram? Ore agora!
+581 estão orando agora.
Junte-se à corrente de oração.