Pular para o conteúdo
Publicidade

Matayo 18:1-5,10

NTNYBL2025 Nyanja

Yani waliwamkulu pa Ufumu wa Mnungu

1 Ndhawi imeneyo oyaluzidwa adamchata Yesu, adaamfunjha, "Yani uyo wali wamkulu kupitilila wonjhe mu Ufumu wa kumwamba?"

2 Yesu wadamtana mwana wamng’ono ni kumwimika pakati pao, 3 Ndiipo wadaakambila, "Zene nikukambilani, ngati simng’anamuka ni kulingana ni wana waang’onoang’ono, simulowa mu Ufumu wa kumwamba. 4 Waliyonjhe uyo wajhichepecha ngati mwana uyu, nde uyo siwakhale wamkulu mu Ufumu wa kumwamba. 5 Uyo wamlandila mwana wamng’ono ngati uyu kwa jhina langa, wanilandila ine."

Maluko 9:42-48; Luka 17:1-2

Chifani cha mbelele iyo yasowa

10 "Khalani maso! Musamdamdelela mmojhi wa wang’ono yawa, pakuti nikukambilani, atumiki wao a kumwamba siku zonjhe ali pamojhi ni Mnungu.

Em outras traduções

  1. TCCL Abra a Palavra de Deus em Chichewa Contemporâneo

    1 Pa nthawi imeneyo ophunzira anabwera kwa Yesu ndipo anamufunsa kuti, "Wamkulu woposa onse ndani mu ufumu wakumwamba?"

    2 Iye anayitana kamwana kakangʼono ndi kukayimiritsa pakati pawo. 3 Ndipo Iye anati, "Zoonadi, Ine ndikuwuzani kuti ngati simusintha ndi kukhala ngati tiana tatingʼono, simudzalowa konse mu ufumu wakumwamba. 4 Chifukwa chake, aliyense amene adzichepetsa yekha ngati kamwana aka, ameneyo ndiye wamkulu koposa onse mu ufumu wakumwamba. 5 Ndipo aliyense amene alandira kamwana kakangʼono ngati aka mu dzina langa, alandira Ine.

    10 "Onetsetsani kuti musanyoze mmodzi wa anawa. Pakuti ndikuwuzani kuti angelo awo kumwamba amakhala pamaso pa Atate anga akumwamba nthawi zonse."

Direitos das traduções citadas

Estes versículos te tocaram? Ore agora!

+581 estão orando agora.

Junte-se à corrente de oração.