Pular para o conteúdo
Publicidade

Matayo 18:6,10

NTNYBL2025 Nyanja

Vindhu ivo vimchiticha mundhu wachite machimo

6 "Ngati mundhu waliyonjhe uyo wamchiticha mmojhi wa wana yawa kuchita chimo, idakakhala mbasa kwa mundhu mmeneyo wamangidwe mbhelo mkhosi mwake ni kubizidwa kuchilundu.

Chifani cha mbelele iyo yasowa

10 "Khalani maso! Musamdamdelela mmojhi wa wang’ono yawa, pakuti nikukambilani, atumiki wao a kumwamba siku zonjhe ali pamojhi ni Mnungu.

Em outras traduções

  1. TCCL Abra a Palavra de Deus em Chichewa Contemporâneo

    6 "Koma ngati wina aliyense achimwitsa mmodzi wa ana awa, amene akhulupirira Ine, kuti achimwe, kukanakhala bwino kuti iye amangiriridwe chimwala chachikulu mʼkhosi mwake ndi kumizidwa pansi pa nyanja.

    10 "Onetsetsani kuti musanyoze mmodzi wa anawa. Pakuti ndikuwuzani kuti angelo awo kumwamba amakhala pamaso pa Atate anga akumwamba nthawi zonse."

Direitos das traduções citadas

Estes versículos te tocaram? Ore agora!

+581 estão orando agora.

Junte-se à corrente de oração.